Beruflich Dokumente
Kultur Dokumente
1. Mnyumba mwa Atate ndi mwanga,mnyumba mwa Atate ndi mwanga. 2. Mnyumba mwa Tate ndidzayimba,mnyumba mwa Tate ndidzayimba. 3. Mnyumba mwa Atate ndidzakondwa. 4. Mnyumba mwa Atate ndidzavina.. 5. Mnyumba mwa Atate ndidzakondwa..
NDINASANGALALA
Chorus: Moto,moto wayaka Moto ndi ntchito ya Yesu. Moto,moto wayaka.Tiyimbe Alleluia.Moto wayaka. 1. Abambo apulumuka,moto wayaka Amayi apulumuka ,moto wayaka Tonse tapulumuka
2. Anyamata apulumuka,Atsikana apulumuka, Tonse tapulumuka. 3. Achidakwa apulumuka,Achamba apulumuka.Tonse tapulumuka. 4. Afiti apulumuka,Asinganga apulumuka.Tonse tapulumuka 5. Ansanje apulumuka,Aumbombo apulumuka,Akuba apulumuka,Onama apulumuka,Mahule apulumuka,Adama apulumuka
Opening prayer
CONFESSION: AMBUYE KONZENI 1. Ambuye konzeni : Ambuye konzeni,moyo wanga utumikire Inu. 2. Ndinetu wakuba: Ambuye konzeni,moyo wanga utumikire Inu. 3. Ndinetu wakumwa : Ambuye konzeni,moyo wanga utumikire Inu. 4. Ndinetu wakupha : Ambuye konzeni,moyo wanga utumikire Inu. 5. Ndinetu wozuza : Ambuye konzeni,moyo wanga utumikire Inu.
2. AMBUYE AKUKONDA 1. Ambuye akukonda,Ambuye akukonda,Ambuye akukonda! Alleluai 2. Ambuye andikonda 3. Ambuke atikonda
4. MBUYE YESU MWAYENERA 5. MULUNGU WATHU MBUYE WATHU Chorus: Alleluia, Amen (4x) 1. Mulungu wathu Mbuye wathu mama oh! Oh! Oh! Dzina lanu lalikuli mama oh! Oh! Oh Inabuka mbiri yake mama oh! Oh! Oh. Kumwamba ndi pansi ponse.
2. Litchulidwa ndi tiana mama oh! Oh! Oh! Takuyamba kulankhula mama oh! Oh! Oh! Manyazi agwire Anthu mama oh! Oh! Oh!
QUITE TIME 1. KUMBAH YA MY LORD Kumba Ya My Lord kumbaya (4x) OH Lord Kumbaya 1. Ana anu Atate akupempha Oh Lord Akupempha 2. Ana anu Ambuye akulira.Oh Lord Akulira
TEACHING TIME
Chorus: Mzimu woyera bwerani (2x) muzatilimbitse Patokha sititha (2x) 1. Mzimu wanzeru bwerani 2. Mzimu wozoza bwerani
OFFERTORY 1. NDIDZATAMANDA AMBUYE 1. Ndidzatamanda Oh Yahwe,Masiku onse amoyo wanga Moyo wanga,moyo wanga (4x) masiku amoyo wanga 2. Ndidzayimbira Oh Yahwe
3. Ndidzathokoza Oh Yahwe
1. AMAYI ANGA NDI MARIA 1. Amai anga ndi Maria, Amai abwino, okoma, Andisunga,nasamala Nandidziwa,nandikonda 2. Ndine mwana Wa Maria Ndikondanso Amai anga Nditamanda,Ndipemphera Ndipatsatu mtima wanga
Closing prayer.